Ochemelela a Moyale Barracks FC Akukonzekera Kuyambitsa Umembala
Ochemelela a timu ya Moyale Barracks FC akukonzekera kuyambitsa dongosolo la umembala lomwe cholinga chake ndi kulimbikitsa gulu la ochemelela komanso kuzindikira anthu omwe ndi ochemelela enieni a Kaning’ina Forest…
